Okebiz Video SearchTitle:Fredokiss - Mukanene Ft BFB & Vinjeru
Duration:04:12
Viewed:16,218
Published:09-10-2020
Source:Youtube

Stream Mukanene by Fredokiss.

Produced by Dare Devils.
Beat By BFB

Lyrics.
[Intro: Vinjeru]
Mukanene mukanene
Kaya akutumani, mukanene
basi

[Chorus: BFB]
Mukanene mukanene mukanene (Mukanene)
Mukanene mukanene mukanene (Mukathoke)
Kaya wakutumani, mukanene (Alaa)
Kaya wakunamizani, mukanene (Shupiti)

Yemwe wakutumani, mukanene
Akupwetekesani, mukanene
Mukanene mukanene mukanene (Mukanene)
Mukanene mukanene mukanene (Mukathoke)

[Verse 1: Fredo]
Nde bwelelani mukanene (Eh)
Mwandikanika kumene (Eh)
Kubwela mutabisa nkhope
Kuyenda ndi midima ngati mileme (Eh)

Munabwela ndi ti njomba ka
Mpaka kutumiza khobha ka
Ghetto simasunga zoba ka
Kanene ntchana ali pompa ka

Kundisemela chi nyau (Nyau)
Kubwela ndi ti mihau (Hau)
Mwakumba pasi a galu
Ngati ma bubu mulibe mawu

Mukanene ku MRA
You can tell them how I got paid
Cause I be hustling all day
Nali ndende but I’m okay

I’m on my knees mama drop cry
Conversating with the most high
Ghetto glory so I won’t die
Fake friends wanna know why

Can a young king make moves anymore?
I got everybody scared trynna blow my downfall

[Chorus: BFB]
Mukanene mukanene mukanene (Mukanene)
Mukanene mukanene mukanene (Mukathoke)
Kaya wakutumani, mukanene (Mukanene)
Kaya wakunamizani, mukanene (Mukathoke)

Yemwe wakutumani, mukanene (Mukanene)
Akupwetekesani, mukanene
Mukanene mukanene mukanene (???)
Mukanene mukanene mukanene

[Verse 2: Fredo]
Pitani mukawauze
Zamabodza zisandikhuze
Ntchana Fredo sangaluze (Luze)
Only weapon is the most high (Most high)

Mukanene ku police (Police)
Fredokiss ndiwa peace (Peace)
Young boss with a business (Business)
Sindipanga zau tchisi (Tchisi)

Mukanene ku chipani (Pani)
Kodi chimakhala chani (Chani)
Kumangopeka zi nkhani (Nkhani)
Kapena mwatha ma plan (Plan)

Makape busy pa Fb (Fb)
Two eyes but they can’t see (Can’t see)
Angokupweteketsani (Tsani)
Angokupepeletsani (Tsani)

I’m trynna receive all my blessings (Yeh)
?? spirit of envy (Woo)
Now I see why you hate me (Hate me)
It’s all because God blessed me (Bless me)

Going through hell, devil knocking on my door
Close it in his face, I will never sell my soul

[Bridge: BFB]

Palibe chinthu anzanga, chosatha (Tauze aise)
Palibe chinthu anzanga, chosatha (Palibe)
Nkhale ufumu umene, umatha (Umatha)
Nkhale unyakwawa umene, umatha (Most def)

Nkhale ubusa umene, umatha (Ehe)
Nkhale uPresident umene, umatha (Basop)
Nkhale moyo umene, umatha
Nkhale chitsulo chimene, chimatha (Lets go)

[Chorus: BFB]
Mukanene mukanene mukanene (Mukanene)
Mukanene mukanene mukanene (Mukathoke)
Kaya wakutumani, mukanene (Mukanene)
Kaya wakunamizani, mukanene (Mukanene)

Yemwe wakutumani, mukanene (Mukanene)
Akupwetekesani, mukanene (Mukathoke)
Mukanene mukanene mukanene (Mukathoke)
Mukanene mukanene mukanene (Mukanene)

[Outro: Fredokiss BFB]
Ghetto makaveli up in this
Chi ntchana aise,
Tizingochimangilila kuchimangilila ukuku, chatuluka aise (Hahaha)

Malawi’s most wanted (Hahaha)
Joseph in the bible, anamagidwa
Jesus Christ was arrested aise
Nelson Mandela, Martin Luther, Steve Bicko

Orton Chirwa, Kamuzu Banda, Fredo
Mafana ose amene ali mkati
Mafana ose amene ali mkati
Kaya ndi Chichiri, Maula, Zomba

Mzuzu, ku ndende, ku rumphi
Aliyese amene akuchita kuziwa kuti
Aise uli mkati komano aise sukuyenela kukhala mkati
Jah guide aise

Nthawi yako ikwana aise
Ingoyesesa kuti aise mabondo ako uziwa user aise
Jah Jah amamva aise

[End]

SHARE TO YOUR FRIENDS


Download Server 1


DOWNLOAD MP4

Download Server 2


DOWNLOAD MP4

Alternative Download :SPONSORED
Loading...
RELATED VIDEOS
Fredokiss - Zausilu ft Young Kay and Martse Fredokiss - Zausilu ft Young Kay and Martse
05:11 | 85,709
Fredokiss - African Bride Ft Temwa, Lilia & Ak On Tha Board Directed By Vj Ken Fredokiss - African Bride Ft Temwa, Lilia & Ak ...
03:26 | 45,320
Climax Feat Bucci, Drobizo, Phyzix,Dette Flo,Santiago,K Banton,Mwanache,Nitrix,Drizzle Akazonic, 6th Climax Feat Bucci, Drobizo, Phyzix,Dette Flo,Sa...
05:15 | 15,687
Onesimus - Solomoni ( Official Video ) Onesimus - Solomoni ( Official Video )
03:18 | 153,400
The Fredokiss Miracle “Ghetto Angel” The Fredokiss Miracle “Ghetto Angel”
39:50 | 447
DDG & OG Parker - Hood Melody ft. YoungBoy Never Broke Again (Official Music Video) DDG & OG Parker - Hood Melody ft. YoungBoy Neve...
03:53 | 125,451
Fredokiss - Upeze Njira ft Lulu (Official Video) Fredokiss - Upeze Njira ft Lulu (Official Video)
05:08 | 68,159
Fredokiss - Dadada (Offical Music Video) Fredokiss - Dadada (Offical Music Video)
03:13 | 83,866


coinpayu