Okebiz Video SearchTitle:Namadingo Ft. Giddes Chalamanda - Linny Hoo (Beautiful Music From Africa) Legend Giddes
Duration:08:30
Viewed:1,410,946
Published:09-06-2021
Source:Youtube

#WMJSTUDIO #GiddesChalamanda #LinnyHoo #Namadingo please enjoy the beautiful song from a Legend (We did all the research we could find) make sure your shows your support Thank You Gidesi  Chalamanda  (born 1930), is most commonly known as “Giddes” He is a Malawian acoustic artist. He was born in Chiradzulu in the Southern region of Malawi. He is one of Malawi’s legendary artists. In the lyrics to his song “Buffalo soldier”, he mentions that if he had enough money he would travel to  America. In 2016, with the help of fans, friends and Malawian organizations both in Malawi and in the Malawian Diaspora, he was able to achieve this dream when he traveled to the US with musicians Davis ndi Edgar. He held a concert at the Black Rock Center for the Arts in the “Pulse of Malawi” concert which celebrated Malawian independence day in Germantown MD Linny Hoo (Official Lyrics) LINNY OOH (ORIGINAL LYRICS LINNY OOH LINNY OOH UYU LINNY LERO MWANA AMENEYU MWANA WA NZERU LINNY HOO LINNY LINNY HOO UYU LINNY LERO MWANA AMENEYU MWANA WA NZERU KUKACHAMA M’MAMA WA AAH AAH AMATENG’A TCHACHE KUSETSA PAKHOMO PAKHOMO PA MAYI WACHE KUKACHA M’MAMAWA AAH AAH EARLY MORNING AMATENG’A TCHACHE KUSETSA PAKHOMO PAKHOMO PA MAYI WACHE MAKOLO A LINNY ETI MAKOLO A LINNY AMUYAMIKIRA AKUTI LINNY LERO MWANA AMENEYU MWANA WA NZERU MAKOLO A LINNY MAKOLO A LINNY AMUYAMIKIRA AKUTI LINNY LERO MWANA AMENEYU MWANA WA NZERU LINNY LINNY HOO LINNY HOO LINNY HOO UYU LINNY LERO MWANA AMENEYU MWANA WA NZERU Tintintile, oooh, tintintintitile, oooh, tintalintantanta, oooh, tantintintanta, ooooh LINNY HOO LINNY LINNY HOO UYU LINNY LERO MWANA AMENEYU MWANA WA NZERU A GIDE, GOGO WA NAMADINGO AMUYAMIKIRA AKUTI NAMADINGO MWANA AMENEYU MWANA WA NZERU SIMIKUNAMANA AGOGO NTHAWI ZINA INE NDIMALOTA INE BAMBO ANGA ATANDISIYA NDASALA NDEKHA NTHAWI ZINA INE NTHAWI ZINA INE NDIMALOTA INE BAMBO ANGA ATAMWALIRA NDASALA NDEKHA NKHONDO AMAMA (NKHONDO AMAMA) NKHONDO AMAMA CHALAMANDA OZAFERA MOYENDA WE NKHONDO MAMA HII NKHONDO UNE AMAMA WEE NKHONDO AMAMA CHALAMANDA UZAFERA MOYENDA WE NDANG’OVYA MBIRIYO MBIRIYO MBIRIYO MWAONA LERO NDANG’OVYA MBIRIYO KA MBIRIYO MBIRIYO MWAONA LERO AGIDDES AYIMBA EEH AYIMBA EEH ZOKOMATU MWAONA LERO NDIPO CHALAMANDA AYIMBA EEH AYIMBA EEH ZOKOMATU MWAONA LERO NDAMVA KUTI MWAKWATIRA MWABALA MWANA WOYERA DZINA LAKE MUSOLO EEH MUNAMVA KWA NDANI KUTI MWAKWATIRA NDAMVA KUTI MWAKWATIRA MWABALA MWANA WOYERA DZINA LAKE MUSOLO EEH MNANGOPANGA UNKHOSWA UKWATI NZAKUYITANARI MUSOLO EEH ETI MUSOLO EEH MUSOLO EEH MUSOLO MAYI MUSOLO EEH MUSOLO EEH MUSOLO MAYI MWANA AMENEYI NDI NAAYI AKE NDIKUFUNA NDIPITE NAWO KU UK MAPHUNZIRO ONSE ONSEE AKAPHUZIRE KU UK MAPHUNZIRO ONSE ONSEE AKAPHUZURE KU UK NDAMVA AGOGO NDAMVA KOMA TIMIYEKO CHE MERI CHE MERI KUNALI CHE MERI CHE MERI UUHMMM CHE MERI UUHMMM CHE MERI KUNALI CHE MERI CHE MERI MAMA MWE IYA MERI MWE IYA DARLIE KUNALI CHE MERI HIIIYO IYA MERI MWE IYA DARLIE KUNALI CHE MERI TIMBIYEPO HAKOMA PAJA HIIIYO IYA MERI MWE IYA DARLIE KUNALI CHE MERI AKAFUNA KUNENA NANE AGIDDES AGIDDES AGIDDES AGIDDES INU ABWANA TABWERANI KUNO AKAFUNA KUNENA NANE CHALAMANDA CHALAMANDA CHALAMANDA CHALAMANDA INU ABWANA TABWERANI KUNO AKAFUNA KUNENA NANE AGIDDES AGIDDES AGIDDES AGIDDES INU ABWANA TABWERANI KUNO ZINALI CHONCHO NTHAWI YA NAPOLO NAPOLO IIIH WACHABE NAPOLO IIIH WACHABE NAPOLO WACHABE NAPOLO WACHABE WATENGA INGALAMU, TENG’A ING’ALAMU KUKATAYA KUMCHING’A KUTUMA AKAIDI KUKATOLA POBWERA ADONA NAHRA MAYIWE WACHABE NAPOLO WACHABE NAPOLO WACHABE TIMALIZE NDI BUFFALO SOLDIER BUFFALO SOLDIER BUFFALO TO AMERICA BUFFALO SOLDIER BUFFALO TO AMERICA WHEN I WAS A YOUNG BOY I DREAMED.. TO THERE IN AMERICA WHEN I WAS A YOUNG BOY NGATI INE KA YOUNG BOY I DREAMED.. TO THERE IN AMERICA OYIYOIYOIYO (X12) IF I HAD MUCH MONEY I GO TO SEE INI AMERICA OOH YEAH IF I HAD MUCH MONEY I GO TO SEE INI AMERICA www.thebestoffmusic.nl/reaggae/giddes-chalamanda/

SHARE TO YOUR FRIENDS


Download Server 1


DOWNLOAD MP4

Download Server 2


DOWNLOAD MP4

Alternative Download :SPONSORED
Loading...
RELATED VIDEOS
Who sang Buffalo Soldier first? Bob Marley or Giddes Chalamanda? Who sang Buffalo Soldier first? Bob Marley or G...
12:13 | 352,652
ALPHA BLONDY , JERUSALEM LIVE ❤️😍🙏 ALPHA BLONDY , JERUSALEM LIVE ❤️😍🙏
07:19 | 24,678,946
UB40 Mix - DJ GIAN UB40 Mix - DJ GIAN
17:44 | 7,405,009
We Are The World - Michael Jackson Bruce Springsteen Lionel Richie Diana Ross We Are The World - Michael Jackson Bruce Spring...
07:14 | 29,621,413
Kenny Rogers - The Gambler Kenny Rogers - The Gambler
03:31 | 186,180,827
Patience Namadingo feat Billy kaunda Reggae Mash up Patience Namadingo feat Billy kaunda Reggae Mas...
09:38 | 395,939
Linny Hoo, Live Performance with Fayez and Michael Bundi Linny Hoo, Live Performance with Fayez and Mich...
03:01 | 106,719
BOB MARLEY - AS MELHORES MUSICAS - THE GREATEST HITS BOB MARLEY BOB MARLEY - AS MELHORES MUSICAS - THE GREATEST...
12:31 | 1,813,999

shopee ads

coinpayu